Jeremiah 52:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero mzindawo udaazingidwa ndi zithandozo mpaka chaka cha 11 cha ufumu wa Zedekiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mudzi unazingidwa mpaka chaka cha khumi ndi chimodzi cha mfumu Zedekiya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mzindawo unazingidwa mpaka chaka cha khumi ndi chimodzi cha ulamuliro wa Mfumu Zedekiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mudzi unazingidwa mpaka caka ca khumi ndi cimodzi ca mfumu Zedekiya.