Jeremiah 52:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pa tsiku lachisanu ndi chinai, pa mwezi wachinai wa chaka chimenecho, pamene njala inali itakula kwambiri mumzindamo kotero kuti anthu analibiretu chakudya m'dzikomo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwezi wachinai, tsiku lachisanu ndi chinai la mwezi, njala inavuta m'mudzi, ndipo anthu a m'dziko analibe zakudya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku lachisanu ndi chinayi la mwezi wachinayi njala inakula kwambiri mu mzindamo kotero kuti munalibe chakudya choti anthu nʼkudya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwezi wacinai, tsiku lacisanu ndi cinai la mwezi, njala inabvuta m'mudzi, ndipo anthu a m'dziko analibe zakudya.