Jeremiah 52:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo a ku Babiloni aja atamgwira Zedekiya, adapita naye kwa Nebukadinezara, ku Ribula m'dziko la Hamati. Komweko Nebukadinezarayo adagamula mlandu wa Zedekiya uja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamgwira iye, namtengera kwa mfumu ya ku Babiloni ku Ribula m'dziko la Hamati; ndipo iye anamweruza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anagwidwa napita naye kwa mfumu ya ku Babuloni ku Ribula mʼdziko la Hamati, kumene anagamula mlandu wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamgwira iye, namtengera kwa mfumu ya ku Babulo ku Ribila m'dziko la Hamati; ndipo iye anamweruza.