Jeremiah 6:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake imvani inu anthu a mitundu ina, penyetsetsani, inu mwasonkhana panonu, zimene zidzaŵagwere anthuwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake tamverani, amitundu inu, dziwani, msonkhano inu, chimene chili mwa iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake imvani, inu anthu a mitundu ina; yangʼanitsitsani, inu amene mwasonkhana pano, chimene chidzawachitikire anthuwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace tamverani, amitundu inu, dziwani, msonkhano inu, cimene ciri mwa iwo.