Jeremiah 6:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzauwononga mzinda wa Ziyoni, mzinda wooneka bwino ndi wokongola.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzachotsa mwana wamkazi wa Ziyoni mkazi wokoma ndi wololopoka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi mzinda wa Ziyoni suli ngati msipu wokongola kwambiri, kumene abusa amafikako ndi ziweto zawo?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzacotsa mwana wamkazi wa Ziyoni mkazi wokoma ndi wololopoka.