Jeremiah 6:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akunena kuti, “Onani, anthu a mtundu wina akubwera kuchokera ku dziko lakumpoto. Mtundu wa anthu amphamvu wanyamuka kuchokera mbali zakutalitali za dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova atero, Taona, mtundu wa anthu uchokera kumpoto; ndi mtundu waukulu adzaukitsidwa ku malekezero a dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akunena kuti, “Taonani, gulu lankhondo likubwera kuchokera kumpoto; mtundu wa anthu amphamvu wanyamuka kuchokera kumathero a dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova atero, Taona, mtundu wa anthu ucokera kumpoto; ndi mtundu waukuru adzaukitsidwa ku malekezero a dziko lapansi.