Jeremiah 6:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musayesere kupita ku minda, kapena kuyenda pa mseu, pakuti adani akubwera ndi nkhondo ndipo ponseponse pali mantha okhaokha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usatulukire kumunda, usayenda m'njira; pakuti lupanga la amaliwongo ndi mantha ali m'mbali zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musapite ku minda kapena kuyenda mʼmisewu, pakuti mdani ali ndi lupanga, ndipo ponseponse anthu akuchita mantha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usaturukire kumunda, usayenda m'njira; pakuti lupanga la amaliwongo ndi mantha ali m'mbali zonse.