Jeremiah 6:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo ali ngati siliva wotaya, pakuti Chauta waŵakana.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anthu adzawatcha nthale ya siliva, pakuti Yehova wakana iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo ali ngati siliva wotayidwa, chifukwa Yehova wawakana.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anthu adzawacha nthale ya siliva, pakuti Yehova wakana iwo.