Jeremiah 7:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake mumabwera kudzaima pamaso panga m'Nyumba ino, Nyumba imene imadziŵika ndi dzina langa. Mumanena kuti, ‘Tapulumuka ife,’ koma mumapitirirabe kumangochita zonyansa zonsezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kudza ndi kuima pamaso panga m'nyumba yino, imene itchedwa dzina langa, ndi kuti, Talanditsidwa; kuti muchite zonyansa izi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo kenaka nʼkubwera kudzayima pamaso panga mʼNyumba ino, Nyumba imene imadziwika ndi Dzina langa, inu nʼkumati, ‘Tapulumuka.’ Mwapulumuka kuti muzichitabe zonyansazi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kudza ndi kuima pamaso panga m'nyumba yino, imene ichedwa dzina langa, ndi kuti, Talanditsidwa; kuti mucite zonyansa izi?