Jeremiah 7:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi tsopano Nyumba ino, Nyumba imene imadziŵika ndi dzina langayi, yasanduka phanga lobisalamo mbala zachifwamba, inu mukuwonerera? Mwiniwakene ndaziwona zonsezi,” akuterotu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi nyumba yino, imene itchedwa dzina langa, ikhala phanga la okwatula pamaso panu? Taona, Ine ndachiona, ati Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi Nyumba ino imene imadziwika ndi Dzina langa, yasanduka phanga la anthu olanda zinthu anzawo mwachifwamba inu mukuona? Komatu ndakhala ndi kuziona zonsezi! akutero Yehova.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi nyumba yino, imene ichedwa dzina langa, ikhala phanga la okwatula pamaso panu? Taona, Ine ndaciona, ati Yehova.