Jeremiah 7:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pitani ku malo anga ku Silo, malo amene poyamba ankadziŵika ndi dzina langa. Mukaone zimene ndidachita kumeneko chifukwa cha kuipa kwa anthu anga Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pitani tsopano kumalo anga amene anali m'Silo, m'mene ndinaikamo dzina langa poyamba paja, ndi kuona chimene ndinachitira chifukwa cha zoipa za anthu anga Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Pitani tsopano ku malo anga ku Silo, malo amene poyamba ankadziwika ndi Dzina langa, ndipo mukaone zimene ndinachita kumeneko chifukwa cha kuyipa kwa anthu anga Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pitani tsopano ku malo anga amene anali m'Silo, m'mene ndinaikamo dzina langa poyamba paja, ndi kuona cimene ndinacitira cifukwa ca zoipa za anthu anga Israyeli.