Jeremiah 7:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakuchotsani pamaso panga monga momwe ndidachotsera abale anu onse, zidzukulu zonse za Efuremu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzakuchotsani inu pamaso panga, monga ndinachotsa abale anu onse, mbeu zonse za Efuremu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakuthamangitsani pamaso panga, ngati momwe ndinachitira abale anu onse, anthu a Efereimu.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzakucotsani inu pamaso panga, monga ndinacotsa abale anu onse, mbeu zonse za Efraimu.