Jeremiah 7:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amati atani! Amayesa kuti akuvuta Ine, koma akungodzivuta okha ndi kumadzichititsa manyazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi autsa mkwiyo wanga? Ati Yehova; kodi sadziutsira okha manyazi a nkhope zao?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma kodi akuvutitsa Ine? Kodi sakungodzivuta okha, ndi kudzichititsa manyazi? akutero Yehova.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi autsa mkwiyo wanga? ati Yehova; kodi sadziutsira okha manyazi a nkhope zao?