Jeremiah 7:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ndidatulutsa makolo anu ku dziko la Ejipito, sindidaŵalamule kuti azipereka nsembe zopsereza kapena nsembe zina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti sindinanena kwa makolo anu, tsiku lija ndinawatulutsa m'dziko la Ejipito, ngakhale kuwauza nsembe zopsereza kapena zophera;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti pamene ndinatulutsa makolo anu ku Igupto ndi kuyankhula nawo, sindinawalamulire kuti azipereka nsembe zopsereza kapena nsembe zinazo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti sindinanena kwa makolo anu, tsiku lija ndinawaturutsa m'dziko la Aigupto, ngakhale kuwauza nsembe zopsereza kapena zophera;