Jeremiah 7:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake udzaŵauze kuti, ‘Uwu ndi mtundu wa anthu uja sadamvere mau a Chauta Mulungu wao, ndipo sadafune kukonzeka. Mau oona atheratu ndipo pakamwa pamangonena zonama zokhazokha.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo udzati kwa iwo, Umene ndi mtundu wosamvera mau a Yehova Mulungu wao, wosalola kulangizidwa, choonadi chatha, chadulidwa pakamwa pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake udzawawuze kuti, ‘Uwu ndi mtundu wa anthu umene sunamvere Yehova Mulungu wake, wosalola kulangizidwa. Choonadi chatha; chazimirira pa milomo yawo.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo udzati kwa iwo, Umene ndi mtundu wosamvera mau a Yehova Mulungu wao, wosalola kulangizidwa, coonadi catha, cadulidwa pakamwa pao.