Jeremiah 7:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mitembo ya anthu ameneŵa idzakhala chakudya cha mbalame zamumlengalenga ndi zilombo zakuthengo. Ndipo palibe wina amene adzazipirikitse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mitembo ya anthu awa idzakhala zakudya za mbalame za mlengalenga, ndi za zilombo za dziko lapansi; palibe amene adzaziopsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mitembo ya anthu amenewa idzakhala chakudya cha mbalame zamlengalenga ndi zirombo zakuthengo, ndipo palibe wina amene adzazipirikitse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mitembo ya anthu awa idzakhala zakudya za mbalame za mlengalenga, ndi za zirombo za dziko lapansi; palibe amene adzaziopsa.