Jeremiah 7:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Konzani makhalidwe anu ndi zochita zanu. Muzichitirana zolungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mukakonzatu njira zanu ndi machitidwe anu; ndi kuweruzatu milandu ya munthu ndi mnansi wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati mutasinthadi makhalidwe anu ndi zochita zanu, ndi kumachitirana zolungama,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mukakonzatu njira zanu ndi macitidwe anu; ndi kuweruzatu milandu ya munthu ndi mnansi wace;