Jeremiah 8:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kudandaula kwanga nkosalekeza. Mtima wanga walefukiratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ha, ndikadatonthoza mtima wanga kuletsa chisoni chake? Mtima wanga walefuka m'kati mwa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndadzazidwa ndi chisoni kwambiri, mtima wanga walefukiratu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ha, ndikadatonthoza mtima wanga kuletsa cisoni cace! mtima wanga walefuka m'kati mwa ine.