Jeremiah 8:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ku Giliyadi kulibe mankhwala ochiritsa? Kodi kumeneko kulibe sing'anga? Chifukwa chiyani mabala a anthu anga sadapole?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi mulibe vunguti m'Giliyadi? Kodi mulibe sing'anga m'menemo; analekeranji kuchira mwana wamkazi wa anthu anga?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ku Giliyadi kulibe mankhwala ochiritsa? Kodi kumeneko kulibe singʼanga? Nanga chifukwa chiyani mabala a anthu anga sanapole?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi mulibe bvunguti m'Gileadi? Kodi mulibe sing'anga m'menemo; analekeranji kucira mwana wamkazi wa anthu anga?