Jeremiah 9:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kukumveka kulira kwa Ziyoni, akuti, “Kalanga ife! Taonongeka! Manyazi aakulu atigwera. Tiyenera kusiya dziko lathu, chifukwa nyumba zathu azigwetsa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mau a kulira amveka m'Ziyoni, Tafunkhidwa, tanyazitsidwa, pakuti tasiya dziko, pakuti agwetsa zokhalamo zathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kulira mwachisoni kukumveka kuchokera mu Ziyoni akuti, ‘Aa! Ife tawonongeka! Tachita manyazi kwambiri! Tiyenera kuchoka mʼdziko lathu chifukwa atipirikitsa mʼnyumba zathu.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mau a kulira amveka m'Ziyoni, Tafunkhidwa, tanyazitsidwa, pakuti tasiya dziko, pakuti agwetsa zokhalamo zathu.