Jeremiah 9:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndani adzandipatse pogona m'chipululu, kuti ndiŵasiye anthu anga ndi kuŵathaŵa. Paja onsewo ngachigololo, ndiponso ndi gulu la anthu onyenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ha, ndikadakhala ndi chigono cha anthu aulendo m'chipululu; kuti ndisiye anthu anga, ndiwachokere, pakuti onse ali achigololo, msonkhano wa anthu achiwembu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndani adzandipatsa malo ogona mʼchipululu kuti ndiwasiye anthu anga ndi kuwachokera kupita kutali; pakuti onse ndi achigololo, ndiponso gulu la anthu onyenga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ha, ndikadakhala ndi cigono ca anthu aulendo m'cipululu; kuti ndisiye anthu anga, ndiwacokere, pakuti onse ali acigololo msonkhano wa anthu aciwembu.