Jeremiah 9:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imfa yatifikira kudzera m'mawindo, yaloŵa ngakhale m'nyumba zathu zaufumu. Idapha ana athu m'miseu, ndipo idatha anyamata m'mabwalo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti imfa yakwera m'mazenera athu, yalowa m'nyumba mwathu; kuchotsa ana kubwalo, ndi anyamata kumiseu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Imfa yatifikira kudzera mʼmazenera athu ndipo yalowa mʼnyumba zathu zotetezedwa; yapha ana athu mʼmisewu, ndi achinyamata athu mʼmabwalo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti imfa yakwera m'mazenera athu, yalowa m'nyumba mwathu; kucotsa ana kubwalo, ndi: anyamata kumiseu.