Job 1:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lina ana aamuna ndi ana aakazi a Yobe ankachita phwando m'nyumba mwa mkulu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono panali tsiku loti ana ake aamuna ndi aakazi analinkudya ndi kumwa vinyo m'nyumba ya mkulu wao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lina pamene ana aamuna ndi ana aakazi a Yobu ankachita phwando ndi kumwa vinyo mʼnyumba mwa mkulu wawo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono panali tsiku loti ana ace amuna ndi akazi analinkudya ndi kumwa vinyo m'nyumba ya mkuru wao;