Job 1:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye kudafika wamthenga kwa Yobe kudzamuuza kuti, “Ng'ombe zinalikulima, ndipo abulu analikudya pafupi pomwepo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nafika mthenga kwa Yobu, nati, Ng'ombe zinalikulima, ndi abulu akazi analikudya pambali pao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
wamthenga anabwera kwa Yobu ndipo anati, “Ngʼombe zanu zotipula ndipo abulu anu amadya chapafupi pomwepo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nafika mthenga kwa Yobu, nati, Ng'ombe zinalikulima, ndi aburu akazi analikudya pambali pao;