Job 1:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyo mau akali m'kamwa, padafikanso wina, nati, “Ana anu onse anali pa phwando m'nyumba ya mkulu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akali chilankhulire, anadza winanso, nati, Ana anu aamuna ndi aakazi analinkudya ndi kumwa vinyo m'nyumba ya mkulu wao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyeyo akuyankhulabe, panafikanso wamthenga wina nati, “Ana anu aamuna ndi aakazi amachita phwando ndi kumwa vinyo mʼnyumba ya mkulu wawo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akali cilankhulire, anadza winanso, nati, Ana anu amuna ndi akazi analinkudya ndi kumwa vinyo m'nyumba ya mkuru wao;