Job 1:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale zidaayenda motero, Yobe sadachimwe kapena kunena kuti, “Mulungu walakwa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa ichi chonse Yobu sanachimwe, kapena kunenera Mulungu cholakwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mu zonsezi, Yobu sanachimwe kapena kunena kuti, “Mulungu walakwa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwa ici conse Yobu sanacimwa, kapena kunenera Mulungu colakwa.