Job 1:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana ake aamuna ankachita phwando mosinthana, tsiku lina kwa wina, tsiku lina kwa wina. Ndipo ankaitana alongo ao atatu aja ku maphwando aowo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana ake amuna anamuka kukachita madyerero m'nyumba ya yense pa tsiku lake; natumiza mthenga kuitana alongo ao atatu adzadye nadzamwe nao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana ake aamuna ankachita phwando mosinthanasinthana mʼnyumba zawo, ndipo ankayitana alongo awo atatu aja kudzadya ndi kumwa nawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana ace amuna anamuka kukacita madyerero m'nyumba ya yense pa tsiku lace; natumiza mthenga kuitana alongo ao atatu adzadye nadzamwe nao.