Job 10:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndithudi, ndatopa nawo moyo wanga, choncho ndidzalankhula zodandaula zanga momasuka. Ndidzaulula zoŵaŵa zonse zamumtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima wanga ulema nao moyo wanga, ndidzadzilolera kudandaula kwanga, ndidzalankhula pakuwawa mtima wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ine ndatopa nawo moyo wanga; choncho ndidzanena zodandaula zanga momasuka ndipo ndidzayankhula mwa kuwawidwa mtima kwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima wanga ulema nao moyo wanga, Ndidzadzilolera kudandaula kwanga, Ndidzalankhula pakuwawa mtima wanga.