Job 10:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudandipatsa moyo mwa chikondi chanu chosasinthika, mudandisamala bwino kuti moyo wanga ulimbike.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwandipatsa moyo, ndi kundikomera mtima, ndi masamalidwe anu anasunga mzimu wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munandipatsa moyo ndi kundionetsa chifundo chanu, ndipo munasamalira bwino moyo wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwandipatsa moyo, ndi kundikomera mtima, Ndi masamalidwe anu anasunga mzimu wanga.