Job 10:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi yonseyo munkabisa zolinga zanu. Koma tsopano ndikuŵadziŵa maganizo anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma izi munazibisa mumtima mwanu; ndidziwa kuti ichi muli nacho.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma izi ndi zimene munabisa mu mtima mwanu, ndipo ndikudziwa kuti zinali mʼmaganizo anu:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma izi munazibisa mumtima mwamu; Ndidziwa kuti ici muli naco: