Job 10:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munkapenyetsetsa kuti muwone ngati nditi ndichimwe. Munali wosafuna kukhululukira tchimo langa lililonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikachimwa mundipenya; ndipo simudzandimasula mphulupulu yanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuti ngati ndingachimwe mudzakhala mukundipenyetsetsa ndipo kuti simudzalola kuti ndisalangidwe chifukwa cha kulakwa kwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikacimwa mundipenya; Ndipo simudzandimasula mphulupulu yanga.