Job 10:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukandipeza wolakwa, tsoka langa! Ngakhale mundipeze wosalakwa, ndigwetsabe nkhope, pakuti ndagwidwa ndi manyazi, poona mavuto angaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikakhala woipa, tsoka ine; ndikakhala wolungama, sindidzakweza mutu wanga; ndadzazidwa ndi manyazi, koma penyani kuzunzika kwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati ndili wolakwa, tsoka langa! Koma ngakhale ndili wosalakwa sindingathe kutukula mutu wanga, pakuti ndagwidwa ndi manyazi ndipo ndamizidwa mʼmavuto anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikakhala woipa, tsoka ine; Ndikakhala wolungama, sindidzakweza mutuwanga; Ndadzazidwa ndi manyazi, Koma penyani kuzunzika kwanga.