Job 10:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikadzilimbitsa mtima, mumakhala ngati mkango wondisaka, mumafuna kundiwopsa ndi mphamvu zanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mutu wanga ukadzikweza, mundisaka ngati mkango; mubweranso ndi kudzionetsera modabwitsa kwa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ndikatukula mutu wanga, Inu mumandisaka ngati mkango ndiponso mumandiopseza ndi mphamvu yanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mutu wanga ukadzikweza, mundisaka ngati mkango; Mubweranso ndi kudzionetsera modabwiza kwa ine.