Job 10:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumandiikiranso mboni zondineneza, mkwiyo wanu umanka nukulirakulira. Magulu anu olimbana nane akunka nachulukirachulukira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundikonzeranso mboni zonditsutsa, ndi kundichulukitsira mkwiyo wanu; nkhondo yobwerezabwereza yandigwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mumabweretsa mboni zatsopano potsutsana nane ndipo mkwiyo wanu pa ine umanka nukulirakulira ndi magulu anu olimbana nane amanka nachulukirachulukira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundikonzeranso mboni zonditsutsa, Ndi kundicurukitsira mkwiyo wanu; Nkhondo yobwereza-bwereza yandigwera.