Job 10:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Inu Mulungu, chifukwa chiyani mudandibadwitsa ineyo? Achikhala ndidaangofa, wina aliyense asanandiwone.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero munandibadwitsa chifukwa ninji? Mwenzi nditapereka moyo wanga, lisanandione diso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Chifukwa chiyani Inu munalola kuti ndibadwe? Ndi bwino ndikanafa diso lililonse lisanandione.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero munandibadwitsa cifukwa ninji? Mwenzi nditapereka moyo wanga, lisanandione diso.