Job 10:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzauza Mulungu kuti, Inu Mulungu, musandiweruze kuti ndine wolakwa. Koma mundidziŵitse chifukwa chimene mukukanganirana nane.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzati kwa Mulungu, Musanditsutse; mundidziwitse chifukwa cha kutsutsana nane.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzati kwa Mulungu wanga: Musandiweruze kuti ndine wolakwa, koma mundiwuze chifukwa chimene Inu mukukanganira ndi ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzati kwa Mulungu, Musanditsutse; Mundidziwitse cifukwa ca kutsutsana nane.