Job 10:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndisanapite kumene sindidzabwerako, dziko la imfa, kumene kuli mdima wandiweyani,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndisanachoke kunka kumene sindikabweranso, ku dziko la mdima ndi la mthunzi wa imfa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndisanapite ku malo amene munthu sabwererako ku dziko la imfa ndi kwa mdima wandiweyani,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndisanacoke kumka kumene sindikabweranso, Ku dziko la mdima ndi la mthunzi wa imfa;