Job 10:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ku dziko lamdimatu ndi lachisokonezo, kumene ngakhale kuŵala kudasanduka mdima.” Zofari
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dziko la mdima bii ngati mdima wandiweyani, dziko la mthunzi wa imfa losalongosoka, kumene kuunika kukunga mdima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ku dziko la mdima wandiweyani ndi chisokonezo, kumene kuwala kumakhala ngati mdima.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dziko la mdima bii ngati mdima wandiweyani, Dziko la mthunzi wa imfa losalongosoka, Kumene kuunika kukunga mdima.