Job 10:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi inu zikukukomerani kuti mundizunze ndi kundinyoza ine, ntchito ya manja anune, chonsecho mukukondera upo wa anthu oipa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chikukomerani kodi kungosautsa, kuti mupeputsa ntchito yolemetsa manja anu, ndi kuti muwalira pa uphungu wa oipa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi mumakondwera mukamandizunza, kunyoza ntchito ya manja anu, chonsecho mukusekerera ndi zochita za anthu oyipa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cikukomerani kodi kungosautsa, Kuti mupeputsa nchito yolemetsa manja anu, Ndi kuti muwalira pa uphungu wa oipa?