Job 10:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi masiku anu ndi aafupi monga m'mene aliri masiku a munthu? Kodi zaka zanu zili ngati zaka za munthu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku anu akunga masiku a munthu kodi, zaka zanu zikunga masiku a munthu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi masiku anu ali ngati masiku a munthu, kapena zaka zanu ngati zaka za munthu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku anu akunga masiku a munthu kodi, Zaka zanu zikunga masiku a munthu;