Job 10:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chiyani tsono mukufufuza zolakwa zanga? Chifukwa chiyani mukufuna kundipeza mlandu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti mufunsa mphulupulu yanga, ndi kulondola choipa changa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti Inu mufufuze zolakwa zanga ndi kulondola tchimo langa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti mufunsa mphulupulu yanga, Ndi kulondola coipa canga;