Job 10:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma chonsecho mukudziŵa bwino lomwe kuti ine ndine wosalakwa, kuti palibe ndi mmodzi yemwe amene angandipulumutse m'manja mwanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chinkana mudziwa kuti sindili woipa, ndipo palibe wakupulumutsa m'dzanja lanu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngakhale mukudziwa kuti sindine wolakwa ndiponso kuti palibe amene angandilanditse mʼdzanja lanu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinkana mudziwa kuti sindiri woipa, Ndipo palibe wakupulumutsa m'dzanja lanu?