Job 10:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mudandiwumba ndi kundipanga ndi manja anu. Koma tsopano mukufuna kundiwononga ndi manja anu omwewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Manja anu anandiumba, nandiulunga monsemu, koma mufuna kundiononga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Munandiwumba ndi kundipanga ndi manja anu. Kodi tsopano Inu mudzatembenuka ndi kundiwononga?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Manja anu anandiumba, nandiulunga monsemu, Koma mufuna kundiononga.