Job 10:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musaiŵale kuti paja mudandipanga ndi dothi. Kodi mukufuna kundibwezeranso kufumbi komweko?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukumbukire kuti mwandiumba ngati dothi; ndipo kodi mudzandibwezera kufumbi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumbukirani kuti munandipanga ndi dothi, kodi tsopano mundibwezeranso ku fumbi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukumbukile kuti mwandiumba ngati dothi; Ndipo kodi mudzandibwezera kupfumbi?