Job 11:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe Yobe, mumtima mwako ukhale wolungama, upemphe chifundo kwa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ukakonzeratu mtima wako, ndi kumtambasulira Iye manja ako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma ngati upereka mtima wako kwa Iye ndi kutambasulira manja ako kwa Iyeyo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ukakonzeratu mtima wako, Ndi kumtambasulira Iye manja ako;