Job 11:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati mumtima mwako muli cholakwa, uchichotse, choipa chilichonse chisakhale m'moyo mwako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukakhala mphulupulu m'dzanja lako, uichotseretu kutali, ndi chisalungamo chisakhale m'mahema mwako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngati utaya tchimo limene lili mʼdzanja lako ndi kusalola choyipa kuti chikhale mʼmoyo mwako,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukakhala mphulupulu m'dzanja lako, uicotseretu kutali, Ndi cisalungamo cisakhale m'mahema mwako;