Job 11:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo moyo wako udzaŵala kupambana dzuŵa. Usiku udzakhala ngati usana kwa iwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo moyo wako udzayera koposa usana; kungakhale kuli mdima kudzakhala ngati m'mawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Moyo wako udzawala kupambana usana, ndipo mdima udzakhala ngati mmawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo moyo wako udzayera koposa usana; Kungakhale kuli mdima kudzakhala ngati m'mawa.