Job 11:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu oipa nawonso adzafunafuna thandizo, koma sadzaona njira yopulumukira, chiyembekezo chao ndi imfa basi.” Yobe
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma maso a oipa adzagoma, ndi pothawirapo padzawasowa, ndipo chiyembekezo chao ndicho kupereka mzimu wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu oyipa adzafuna thandizo osalipeza, ndipo adzasowa njira yothawirapo; chiyembekezo chawo chidzakhala imfa basi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma maso a oipa adzagoma, Ndi pothawirapo padzawasowa, Ndipo ciyembekezo cao ndico kupereka mzimu wao.