Job 11:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe umati mau akowo ndi oona, ukuti ndiwe wangwiro pamaso pa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti unena, Chiphunzitso changa nchoona, ndipo ndili woyera pamaso pako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe ukunena kwa Mulungu kuti, ‘Zikhulupiriro zanga ndi zopanda zolakwika ndipo ndine wangwiro pamaso panu.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti unena, Ciphunzitso canga ncoona, Ndipo ndiri woyera pamaso pako.