Job 11:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ha, achikhala Mulungu adaalankhula, achikhala adaakudzudzula,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma, ha? Mwenzi atanena Mulungu, ndi kukutsegulira milomo yake motsutsa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aa, nʼkanakonda Mulungu akanayankhula kuti Iye atsekule pakamwa pake kutsutsana nawe
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma, hal mwenzi atanena Mulungu, Ndi kukutsegulira milomo yace motsutsa;